Maso By Langwan Piksy

Lyrics Of Maso from MASO

VERSE 1
Ndakhalilidwa
Ndakankhidwa
Ndakanidwa
Ndasalidwa
Ndapanidwa
But I didn’t go down
Yeah ena ankati sindingazithe
Malo ena sinnapite
Zinawawa koma look at me now
Ey
You know, nthawi zina tima manga ndende tokha
Zabwino zochulukitsa tokha tima blocker
Timafuna zophweka zikavuta tima dropper
Kudikira ena ayambe ife tingokopa
Anthu ochuluka they wanna see me begging
Kuyamba ngati othandiza they wanna leave me hanging
Pankhope ngati a chifundo but I know they faking
Pankhope a chikondi kumbaliko nde ndisekeni
People take your kindness for a weakness
Kusiya zawo uko they mind your business
You know, sometimes ndi bwino kumasunga chinsinsi
Kukhala wekha bola mu mtima wako muli peace
(amen)

CHORUS

So many things I can thank god for
Madalitso ndaona ndi maso
Anali nane pompo
Pomwe panali khoma anayikapo khomo
Yeah
So many things I can thank God for
Madalitso ndawaona ndi maso
Zomwe ankati sizingandichitikire
Ndaziona ndi maso

VERSE 2
Musanandide mufunse komwe ndachoka
Mukanakhala ine ena a inu mukanafoka
I lost hope
It got too hard to cope
Everything felt so wrong
Man it’s been….hard for me
Maloto far from real
Lero mphamvu ndzipeza ain no stopping me
Ndingati ku maloto nkamaona success
Onse munayima nane nyengo iyi God bless
Whoever thought ndidzafika this far?
Ndinali mnyamata pano ndi Mister
Anthu ochuluka callin’ me star
Nsanje ayi mudzinditcha victor
Lero zinthu zimasintha when I step in
Mphepo ingadze molimba im not shaken
Ndimangoseka
Zikuphweka
Mulungu wadalitsa zonse zongotheka

CHORUS
So many things I can thank god for
Madalitso ndaona ndi maso
Anali nane pompo
Pomwe panali khoma anayikapo khomo
Yeah
So many things I can thank God for
Madalitso ndawaona ndi maso
Zomwe ankati sizingandichitikire
Ndaziona ndi maso

VERSE 3
Anthu amene andikondane zeni zeni
(ndawaona ndi maso)
Adani anga onse ali pa ntetete
(ndawaona ndi maso)
Chisomo chanu position kuchita maintain
(ndachiona ndi maso)
Chikondi ndachiona ndi maso…maso…maso

CHORUS

So many things I can thank god for
Madalitso ndaona ndi maso
Anali nane pompo
Pomwe panali khoma anayikapo khomo
Yeah
So many things I can thank God for
Madalitso ndawaona ndi maso
Zomwe ankati sizingandichitikire
Ndaziona ndi maso

Song Details

Album/Movie: MASO
Artist: Langwan Piksy
Music Director: Langwan Piksy
Viewed (total): 229 times

Report Correction?

(Not Rated Yet)
 

Other Lyrics from MASO album

Mphongo
Ngini Bho
Uncle Short One
Ponya Mwendo
Kuzizira
Appettizer
Bambo Nyimbo

Search Lyrics
e.g. fortress, eminem, britney spears

Top 10 Lyrics by Langwan Piksy

1 - MASO - Maso
2 - MASO - Mphongo
3 - MASO - Ngini Bho
4 - MASO - Ponya Mwendo
5 - MASO - Uncle Short One
6 - MASO - Appettizer
7 - MASO - Bambo Nyimbo
8 - MASO - Kuzizira

Latest Additions

Feral
Turn Me Back
Conscious
Philippine Geography
Five Minutes
War Of Hormone
Unspoken
Tonight You're Perfect
Thrive
The Parable