Ngini Bho By Langwan Piksy

Lyrics Of Ngini Bho from MASO

#Ndefeyo entertainment
Kufeela ngati nsomba….fresh
Zoti zikutheka zosavuta kupanga trace
Yes
Sangapange catch yanga pace
Press
Ili nkati ati ndiyichite address
Luso ndi asset – fixed
That is why pa izi I’m a beast
Consider this
Truth, not a diss
Shame..I can’t find your names on the list
Ngati industry yi ndi matabwa I’m the carpenter
Ngati industry ndi ma days I’m the calendar
Ma guy amadziwa sindimaopa ku challenger
Nyumba yanga si ya magalasi nde ndima genda
Muli sick? Ndikuchiritsani
Ndimadula mapiko muli fly ndikutsitsani
Ndimazidabwa ndekha nde ndimazigomera
I’m so blessed pena pake ndimazihopela

HOOK

Bho
Ngini ili bho
Ziri bho
Ngini ili bho
Akuti ngini sili bho ndine amene ndiri bho
Chifukwa ndine amene ndikumangothoka thoka kuti ngini ili bho
Ngini ili bho!

VERSE TWO
Langwan mu studio you know the game is on
Ndi chi confidence chokwana you know the war is won
You got issues? Get off my zone
Nzosayankhulika zomwe iwe ungazione
Kumenya hit after hit
Afana ongoyesa sakuchedwa kupanga quit
Ey y’all you got none to say you better sit
Ati ndimalemba nyimbo ngati mfiti
Ih kaya
Munkatokotatu pano muli quite
Kapena ka luso kanu kali pa diet?
Tinayamba pa kale anzanu sitiguga
Moyo ndi owawa anzanu timabwira sugar
Nkaziona nkhope zawo ndiona mkwiyo
Nyimbo zawo ngati nsima yopanda ndiwo
Akafuna kuthoka zomwe athoka ndinathoka prior
Nyimbo ndilo bed langa ma rhymes ndi pillow

HOOK
Ngini ili bho
Ziri bho
Ngini ili bho
Akuti ngini sili bho ndine amene ndiri bho
Chifukwa ndine amene ndikumangothoka thoka kuti ngini ili bho
Ngini ili bho!

VERSE THREE

I make my hommies proud, one of them made it
They can’t hold the joy - so they go spread it
It doesn’t please some - so we let them hate it
They can only hate it, but they can’t end it
They start beef so they could get famous
I already rock earth maybe you can try Venus
On my way still heading for the top
Yeah fans imandifeela ati PIKSY uli dope
HOOK

Song Details

Album/Movie: MASO
Artist: Langwan Piksy
Music Director: Langwan Piksy
Viewed (total): 236 times

Report Correction?

(Not Rated Yet)
 

Other Lyrics from MASO album

Maso
Mphongo
Uncle Short One
Ponya Mwendo
Kuzizira
Appettizer
Bambo Nyimbo

Search Lyrics
e.g. fortress, eminem, britney spears

Top 10 Lyrics by Langwan Piksy

1 - MASO - Uncle Short One
2 - MASO - Maso
3 - MASO - Mphongo
4 - MASO - Ngini Bho
5 - MASO - Ponya Mwendo
6 - MASO - Appettizer
7 - MASO - Bambo Nyimbo
8 - MASO - Kuzizira

Latest Additions

Feral
Turn Me Back
Conscious
Philippine Geography
Five Minutes
War Of Hormone
Unspoken
Tonight You're Perfect
Thrive
The Parable