Uncle Short One By Langwan Piksy

Lyrics Of Uncle Short One from MASO

Chi Piksy Chinfarner Chodziwiker Ndi Boumurr
CHORUS
Hey Uncle
Uncle Short-one
Mukuganizira zotani
Uncle Short-one
Kuno ngini yakuphonyani
Uncle Short-one
Ndikale lija munatchona inu
Uncle Short-one
Kuno mbumba yakusowani
VERSE ONE
Maloto awa tinayambira limodzi
Sitinaganizire zinthu zingafike chonchi
Mmaso mwa ine ya chimwemwe misonzi
Oh I wish mukanakhala kuno nkozi
My uncle komanso my best friend
Munkandiuza chirichonse munali open
Ndinkadzanena kwa inu ndikayiputa ndeu
Kamunthu kakafupi koma simakani akewo
Pena ndimaseka……ndekha
Munkati mukakwiya munkadzitchula undertaker
Nkhani za inu zambiri zongopeka
Pano ndinakula munkathoka ngini yosatheka
(Laugh)
I called you biggie
Munali nane olo weather ingakhale windy
Muzambiri munandipanga lead
I'm a man now pano ndidziwa zambiri
CHORUS
VERSE TWO
Munkanena kuti zinthu zidzayenda
One day….dollar ndidza spenda
Munkanena ndidzaphula if I work hard
One day… zakale ndidzagenda
Ndikakhala duuu
Kukumbuka kale lathu
Tinkasowa zinthu
Munaganizano zongotuuu... luka
Koma zonse munanena sindinazitaye
Ngakhale ngini inashupa sindinagwe mphwayi
Mulungu anandidalitsa inakwana nthawi
Kunyada kwa abambo anga chimwemwe cha mayi
Ngini bho panopa I’m doing awesome
Pano ndinapeza aine ma bouncer
Pamene pankawopsapo pano ndinadutsa
Mulungu anachotsa zonse zinkasautsa
CHORUS
VERSE THREE
Ndikasekelera ndinuyo ndimakumbukira
Ndikanakondwera mukanakhala mwafupikira
Kwa inu… zambiri ndinaphunzira
Munkandiuza madalitso adzandikhuthukira
Mukanakhalapo mukanamva kukoma
Nephew wanu akudziwika ndi boma
Anakula pano anapeza kadona
Uncle…nephew wanu anablowa
Success yanga inabwera ngati heart attack
Ndikanena zinthu amayesa ndikulalata
Luso lija likumabweretsa dollar
Zimene zinkapinga zija Ambuye anathyola
Mulungu anatsegula khomo
Nephew wanu panopa ndi role model
Ndakusowani
Uncle Short-one
Ndine wanu wanu Langwan
CHORUS
Outro
Ndefeyo entertainment

Song Details

Album/Movie: MASO
Artist: Langwan Piksy
Music Director: Langwan Piksy
Viewed (total): 186 times

Report Correction?

(Not Rated Yet)
 

Other Lyrics from MASO album

Maso
Mphongo
Ngini Bho
Ponya Mwendo
Kuzizira
Appettizer
Bambo Nyimbo

Search Lyrics
e.g. fortress, eminem, britney spears

Top 10 Lyrics by Langwan Piksy

1 - MASO - Uncle Short One
2 - MASO - Maso
3 - MASO - Mphongo
4 - MASO - Ngini Bho
5 - MASO - Ponya Mwendo
6 - MASO - Appettizer
7 - MASO - Bambo Nyimbo
8 - MASO - Kuzizira

Latest Additions

Feral
Turn Me Back
Conscious
Philippine Geography
Five Minutes
War Of Hormone
Unspoken
Tonight You're Perfect
Thrive
The Parable