Bambo Nyimbo By Langwan Piksy

Lyrics Of Bambo Nyimbo from MASO

VERSE ONE – PIKSY
Mmudzi uwu anthu amandikonda kwambiri
Amfumu ati ndiime u MP
Ati nyimbo za ine ziri amazing
Pazokha zitha kukwana kukhala ngati incentive
Ku wina u MP no campaign
Opikisana nawo akuchita complain
Kuchipangitsa Chambo kufeela ngati Ncheni
And position yanga ndikuichitabe maintain
Mu nyimbomu, ndikondwera mmenemu
Kunjoya, kunjoyetsa ena ndikupeza revenue
They go hard ndeno I go harder
Instrumental kwa ine imagwada
Okay, let me take you slow
Ndikufuna apa pokha mundimvetse bho
Ati zinthu izi ndimazitha bad
Bamboo nyimbo, nyimbo zimanditcha dad

BRIDGE
Bambo nyimbo
Bambo nyimbo uuuh
VERSE TWO - PIKSY
Ndimanva kukoma ndikamamenya tune
Ochuluka anthu nkumangokuwa nthumwi
Ndingati Christmas yomwe yabwera June
Ndikaona atsuna akugwedeza fandum
Yeah, amanditcha bambo nyimbo
Nyimbo so beautiful rainbow ndi symbol
Osanama zikuyenda bwino moti
Unlike mmbuyo muja pano zafika pa chonchi
Bambo nyimbo timenye nanu single
Nyimbo yanga mungondimenyera intro
Simatama koma kungoyamikira
Mmene zinthu zakhalira
Madalitso ndalandira
Kumenya beats, fans ingofeela
Kumenya ma show ma venue kusefukira
Wina ndi uyu walowera pa window
Ngati ndikunama tandionetse chidindo

Mhm anzawo, mukuona bwa?
CHORUS – JAY J
Ndimatchedwa anzawo a nyimbo
Ndinachokera pa zero
Kufika lero kudziwika ndi dziko aaah
Ndimatchedwa anzawo anyimbo
Ndimatchedwa anzawo a nyimbo
Akufuna chimbale kapena single
Zokondweretsa kudziwika ndi dziko aaah
Ndimatchedwa anzawo a nyimbo
VERSE THREE
HEH!
Ndimatchedwa anzawo a nyimbo
Ngakhalenso mithutha inandipatsa udindo
It's all good you know zabwino bwino
Zonse zikutheka anzawo anyimbo
Yo! Tikupanga zen zen
Bamboo nyimbo anzawo tikumenya yeni yeni
Osafowoka kugwedeza pamalo
Ku holda microphone kukuwa ngati mkango
Ma guy akudziwa
Onse kutifeela
Palibe kugonja nonse mukudziwa
Kumva kukoma kucheza ah uh
Sinthawi yogona no no phada yah!
Keep the fire blazing (yah)
Moto osazima (yah)
Yonse morale
Bambo nyimbo, anzawo anyimbo bluh!

CHORUS – JAY J
Ndimatchedwa anzawo a nyimbo
Ndinachokera pa zero
Kufika lero kudziwika ndi dziko aaah
Ndimatchedwa anzawo anyimbo
Ndimatchedwa anzawo a nyimbo
Akufuna chimbale kapena single
Zokondweretsa kudziwika ndi dziko aaah
Ndimatchedwa anzawo a nyimbo
CHORUS – PIKSY
Amanditcha bambo Nyimbo
Ndinachokera pa zero
Kufika lero kudziwika ndi dziko yeah
Amanditcha bambo Nyimbo aaah
Amanditcha bambo Nyimbo
Ndinachokera pa zero
Akufufuna chimbale kapena single
Zokondweretsa kudziwika ndi dziko aaah
Amanditcha bambo Nyimbo

Song Details

Album/Movie: MASO
Artist: Langwan Piksy
Music Director: Langwan Piksy
Viewed (total): 188 times

Report Correction?

(Not Rated Yet)
 

Other Lyrics from MASO album

Maso
Mphongo
Ngini Bho
Uncle Short One
Ponya Mwendo
Kuzizira
Appettizer

Search Lyrics
e.g. fortress, eminem, britney spears

Top 10 Lyrics by Langwan Piksy

1 - MASO - Mphongo
2 - MASO - Bambo Nyimbo
3 - MASO - Kuzizira
4 - MASO - Maso
5 - MASO - Appettizer
6 - MASO - Ngini Bho
7 - MASO - Ponya Mwendo
8 - MASO - Uncle Short One

Latest Additions

Feral
Turn Me Back
Conscious
Philippine Geography
Five Minutes
War Of Hormone
Unspoken
Tonight You're Perfect
Thrive
The Parable